Ekisodo 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo anthu anayamba kung’ung’udza motsutsana ndi Mose,+ kuti: “Timwa chiyani?” Salimo 106:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Anapitiriza kung’ung’udza m’mahema awo,+Moti sanamvere mawu a Yehova.+ 1 Akorinto 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tisakhalenso ong’ung’udza, mmene ena mwa iwo anang’ung’udzira,+ wowonongayo+ n’kuwawononga onsewo.
10 Tisakhalenso ong’ung’udza, mmene ena mwa iwo anang’ung’udzira,+ wowonongayo+ n’kuwawononga onsewo.