Numeri 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana onse a Isiraeli anayamba kudandaula za Mose ndi Aroni.+ Ndipo khamu lonselo linati: “Zikanakhala bwino tikanangofera ku Iguputo, kapena tikanangofera m’chipululu muno. Numeri 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Kodi khamu la anthu oipa amenewa lidandaula motsutsana nane kufikira liti?+ Ndamva kudandaula konseko kumene ana a Isiraeli akuchita motsutsana nane.+ Deuteronomo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamenepo munapitiriza kung’ung’udza m’mahema mwanu kuti, ‘Yehova anatitulutsa m’dziko la Iguputo+ chifukwa chodana nafe,+ kuti adzatipereke m’manja mwa Aamori kuti atiwononge.+
2 Ana onse a Isiraeli anayamba kudandaula za Mose ndi Aroni.+ Ndipo khamu lonselo linati: “Zikanakhala bwino tikanangofera ku Iguputo, kapena tikanangofera m’chipululu muno.
27 “Kodi khamu la anthu oipa amenewa lidandaula motsutsana nane kufikira liti?+ Ndamva kudandaula konseko kumene ana a Isiraeli akuchita motsutsana nane.+
27 Pamenepo munapitiriza kung’ung’udza m’mahema mwanu kuti, ‘Yehova anatitulutsa m’dziko la Iguputo+ chifukwa chodana nafe,+ kuti adzatipereke m’manja mwa Aamori kuti atiwononge.+