Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 16:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ndipo ana a Isiraeli anadya mana kwa zaka 40+ mpaka pamene analowa m’dziko lokhalidwa ndi anthu.+ Mana ndiwo anali chakudya chawo mpaka pamene anafika m’malire a dziko la Kanani.+

  • Numeri 32:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova anawakwiyira koopsa Aisiraeli ndipo anawachititsa kuzungulira m’chipululu zaka 40,+ mpaka m’badwo wonse wochita zoipa pamaso pa Yehova utatha.+

  • Deuteronomo 8:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Muzikumbukira njira yonse imene Yehova Mulungu wanu anakuyendetsani m’chipululu zaka 40 zonsezi.+ Iye anakuyendetsani m’chipululu kuti akuphunzitseni kudzichepetsa,+ kukuyesani+ pofuna kudziwa zimene zinali mumtima mwanu,+ kuti aone ngati mukanasunga malamulo ake kapena ayi.

  • Salimo 95:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Pamene makolo anu anandiyesa.+

      Iwo anandisanthula, ndipo anaonanso ntchito zanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena