Ekisodo 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Ndikuvumbitsirani mkate kuchokera kumwamba,+ ndipo anthu azipita kukatola. Aliyense azitola muyezo wom’kwanira pa tsikulo.+ Ndikuchita izi kuti ndiwayese ngati adzatsatira chilamulo changa kapena ayi.+ Ekisodo 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musaope, chifukwa Mulungu woona wabwera+ kuti akuyeseni, ndi kuti mupitirizebe kumuopa kuti musachimwe.”+
4 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Ndikuvumbitsirani mkate kuchokera kumwamba,+ ndipo anthu azipita kukatola. Aliyense azitola muyezo wom’kwanira pa tsikulo.+ Ndikuchita izi kuti ndiwayese ngati adzatsatira chilamulo changa kapena ayi.+
20 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musaope, chifukwa Mulungu woona wabwera+ kuti akuyeseni, ndi kuti mupitirizebe kumuopa kuti musachimwe.”+