Nehemiya 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mfumu inapereka lamulo lokhudza oimba,+ ndipo panali dongosolo loti aziwapatsa thandizo tsiku lililonse malinga ndi zofunikira za tsikulo.+ Miyambo 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zachinyengo ndi mawu onama muwaike kutali ndi ine.+ Musandipatse umphawi kapena chuma.+ Ndidye chakudya chimene ndikufunika kudya,+ Mateyu 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mutipatse ife lero chakudya chathu chalero.+
23 Mfumu inapereka lamulo lokhudza oimba,+ ndipo panali dongosolo loti aziwapatsa thandizo tsiku lililonse malinga ndi zofunikira za tsikulo.+
8 Zachinyengo ndi mawu onama muwaike kutali ndi ine.+ Musandipatse umphawi kapena chuma.+ Ndidye chakudya chimene ndikufunika kudya,+