Salimo 78:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo anapitiriza kuwagwetsera mana ngati mvula kuti adye.+Iye anawapatsa tirigu wochokera kumwamba.+ Salimo 105:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anapempha nyama ndipo anawapatsa zinziri,+Anawadyetsa chakudya chochokera kumwamba.+ Yohane 6:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Makolo athu anadya mana+ m’chipululu, monga mmene Malemba amanenera kuti, ‘Anawapatsa chakudya chochokera kumwamba kuti adye.’”+ 1 Akorinto 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiponso, onse anadya chakudya chimodzimodzi chauzimu,+
24 Ndipo anapitiriza kuwagwetsera mana ngati mvula kuti adye.+Iye anawapatsa tirigu wochokera kumwamba.+
31 Makolo athu anadya mana+ m’chipululu, monga mmene Malemba amanenera kuti, ‘Anawapatsa chakudya chochokera kumwamba kuti adye.’”+