Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 16:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ana a Isiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “N’chiyani ichi?” Chifukwa sanadziwe kuti chinali chiyani. Pamenepo Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+

  • Numeri 11:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Manawo+ anali ngati mapira,*+ ndipo maonekedwe ake anali ngati utomoni woonekera mkati ngati galasi.+

  • Nehemiya 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Munawapatsanso mkate wochokera kumwamba kuti athetse njala yawo.+ Munatulutsa madzi pathanthwe ndi kuwapatsa kuti athetse ludzu lawo,+ ndiyeno munawauza kuti alowe+ ndi kutenga dziko limene munalumbira mutakweza dzanja lanu kuti mudzawapatsa.+

  • Yohane 6:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Makolo anu anadya mana+ m’chipululu koma anamwalirabe.

  • 1 Akorinto 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiponso, onse anadya chakudya chimodzimodzi chauzimu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena