Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako mame aja anauma ndipo panthaka ya m’chipululumo panapezeka tinthu topyapyala ndi tolimba+ koma tosalala ngati mame+ amene aundana panthaka.

  • Nehemiya 9:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Munawapatsa mzimu wanu wabwino+ kuti akhale anzeru. Simunawamane mana+ ndipo munawapatsa madzi kuti athetse ludzu lawo.+

  • Yohane 6:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Makolo athu anadya mana+ m’chipululu, monga mmene Malemba amanenera kuti, ‘Anawapatsa chakudya chochokera kumwamba kuti adye.’”+

  • Yohane 6:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Iye wotsika kuchokera kumwamba, amene amapereka moyo kudziko ndiye chakudya chimene Mulungu amapereka.”

  • Yohane 6:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Ine ndine chakudya chamoyo chotsika kumwamba. Ngati wina adyako chakudya chimenechi adzakhala ndi moyo kosatha. Ndipotu chakudya chimene ndidzapereke kuti dzikoli lipeze moyo,+ ndicho mnofu wangawu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena