Ekisodo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Isiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “N’chiyani ichi?” Chifukwa sanadziwe kuti chinali chiyani. Pamenepo Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+
15 Ana a Isiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “N’chiyani ichi?” Chifukwa sanadziwe kuti chinali chiyani. Pamenepo Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+