Numeri 33:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Potsirizira pake ananyamuka kumapiri a Abarimu n’kukamanga msasa ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, m’chipululu cha Mowabu.+ Deuteronomo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Taonani, ndikukupatsani dzikolo. Mukalowe m’dzikolo ndi kulitenga kuti likhale lanu, dziko limene Yehova analumbirira makolo anu, Abulahamu, Isaki+ ndi Yakobo,+ kuti adzalipereka kwa iwo ndi kwa mbewu yawo.’+ Deuteronomo 34:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndiyeno Mose anachoka m’chipululu cha Mowabu kupita m’phiri la Nebo,+ pamwamba pa Pisiga,+ moyang’anana ndi Yeriko.+ Pamenepo Yehova anayamba kumuonetsa dziko lonse, kuchokera ku Giliyadi mpaka ku Dani.+
48 Potsirizira pake ananyamuka kumapiri a Abarimu n’kukamanga msasa ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, m’chipululu cha Mowabu.+
8 Taonani, ndikukupatsani dzikolo. Mukalowe m’dzikolo ndi kulitenga kuti likhale lanu, dziko limene Yehova analumbirira makolo anu, Abulahamu, Isaki+ ndi Yakobo,+ kuti adzalipereka kwa iwo ndi kwa mbewu yawo.’+
34 Ndiyeno Mose anachoka m’chipululu cha Mowabu kupita m’phiri la Nebo,+ pamwamba pa Pisiga,+ moyang’anana ndi Yeriko.+ Pamenepo Yehova anayamba kumuonetsa dziko lonse, kuchokera ku Giliyadi mpaka ku Dani.+