Deuteronomo 34:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako Mose anachoka mʼchipululu cha Mowabu kupita mʼphiri la Nebo,+ pamwamba pa Pisiga,+ moyangʼanizana ndi Yeriko.+ Ndipo Yehova anamuonetsa dziko lonse, kuchokera ku Giliyadi mpaka ku Dani.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:1 ‘Dziko Lokoma’, ptsa. 8-9
34 Kenako Mose anachoka mʼchipululu cha Mowabu kupita mʼphiri la Nebo,+ pamwamba pa Pisiga,+ moyangʼanizana ndi Yeriko.+ Ndipo Yehova anamuonetsa dziko lonse, kuchokera ku Giliyadi mpaka ku Dani.+