20 Atachoka ku Bamoti anafika kuchigwa cha dziko la Mowabu,+ kumalire ndi mzinda wa Pisiga.+ Chitunda cha Pisiga chinayang’anana ndi dera la Yesimoni.+
27 Kwera pamwamba pa Pisiga+ ndi kukweza maso ako, ndipo uyang’ane kumadzulo, kumpoto, kum’mwera ndi kum’mawa, uone dzikolo ndi maso ako, chifukwa suwoloka Yorodano uyu.+