Numeri 26:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Awa ndiwo anthu amene Mose ndi wansembe Eleazara anawawerenga pakati pa ana a Isiraeli. Anawawerengera m’chipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, kufupi ndi Yeriko.+ Numeri 33:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Anakhalabe mumsasa wawo pafupi ndi Yorodano, kuyambira ku Beti-yesimoti+ mpaka ku Abele-sitimu,+ m’chipululu cha Mowabu.
63 Awa ndiwo anthu amene Mose ndi wansembe Eleazara anawawerenga pakati pa ana a Isiraeli. Anawawerengera m’chipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, kufupi ndi Yeriko.+
49 Anakhalabe mumsasa wawo pafupi ndi Yorodano, kuyambira ku Beti-yesimoti+ mpaka ku Abele-sitimu,+ m’chipululu cha Mowabu.