Genesis 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu n’kumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako.”+ Pambuyo pake, iye anamanga pamalopo guwa lansembe la Yehova, yemwe anaonekera kwa iye. Genesis 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Dziko lonse limene ukulionali, ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako, kuti likhale lanu mpaka kalekale.+ Genesis 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Ndidzakwaniritsa pangano langa la pakati pa ine ndi iwe,+ ndi mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe ku mibadwomibadwo. Lidzakhala pangano mpaka kalekale,+ kusonyeza kuti ndine Mulungu wako ndi wa mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe.+
7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu n’kumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako.”+ Pambuyo pake, iye anamanga pamalopo guwa lansembe la Yehova, yemwe anaonekera kwa iye.
15 Dziko lonse limene ukulionali, ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako, kuti likhale lanu mpaka kalekale.+
7 “Ndidzakwaniritsa pangano langa la pakati pa ine ndi iwe,+ ndi mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe ku mibadwomibadwo. Lidzakhala pangano mpaka kalekale,+ kusonyeza kuti ndine Mulungu wako ndi wa mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe.+