Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu n’kumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako.”+ Pambuyo pake, iye anamanga pamalopo guwa lansembe la Yehova, yemwe anaonekera kwa iye.

  • Genesis 15:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+

  • Genesis 24:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova Mulungu wakumwamba, amene ananditenga ine kunyumba kwa bambo anga ndi kudziko la abale anga,+ amenenso anandilankhula ndi kundilumbirira+ kuti, ‘Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako,’+ ameneyo atumiza mngelo wake kuti akutsogolere,+ ndipo kumeneko, ndithu ukam’tengere mwana wanga mkazi.+

  • Ekisodo 33:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ndiyeno Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Nyamukani, muchoke pano, iweyo ndi anthu amene unawatsogolera potuluka m’dziko la Iguputo.+ Mupite kudziko limene ndinalumbira kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo kuti, ‘Ndidzapereka dziko ili kwa mbewu yako.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena