Genesis 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Ndidzachulukitsa mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, ndipo mayiko onsewa ndidzawapereka kwa mbewu yako.+ Mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso*+ ndithu kudzera mwa mbewu yako.’ Machitidwe 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komatu sanam’patse cholowa chilichonse mmenemu ayi, ngakhale kadera kochepetsetsa.+ Koma anamulonjeza kuti adzamupatsa dzikoli monga cholowa chake,+ ndi cha mbewu yake,+ ngakhale kuti pa nthawiyo n’kuti alibe mwana.+ Aheberi 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anali wokonzeka kuchita zimenezo ngakhale kuti anali atauzidwa kuti: “Amene adzatchedwa ‘mbewu yako’ adzachokera mwa Isaki.”+
4 ‘Ndidzachulukitsa mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, ndipo mayiko onsewa ndidzawapereka kwa mbewu yako.+ Mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso*+ ndithu kudzera mwa mbewu yako.’
5 Komatu sanam’patse cholowa chilichonse mmenemu ayi, ngakhale kadera kochepetsetsa.+ Koma anamulonjeza kuti adzamupatsa dzikoli monga cholowa chake,+ ndi cha mbewu yake,+ ngakhale kuti pa nthawiyo n’kuti alibe mwana.+
18 Anali wokonzeka kuchita zimenezo ngakhale kuti anali atauzidwa kuti: “Amene adzatchedwa ‘mbewu yako’ adzachokera mwa Isaki.”+