Genesis 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko limene ukukhalamo ngati mlendoli,+ ndidzalipereka kwa iwe ndi mbewu yako yobwera pambuyo pako. Dziko lonse la Kanani lidzakhala lawo mpaka kalekale, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”+ Ekisodo 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndidzakulowetsani m’dziko limene ndinalumbirira+ Abulahamu, Isaki ndi Yakobo, nditakweza dzanja langa. Ndidzakupatsani dzikolo kukhala lanu.+ Ine ndine Yehova.’”+
8 Dziko limene ukukhalamo ngati mlendoli,+ ndidzalipereka kwa iwe ndi mbewu yako yobwera pambuyo pako. Dziko lonse la Kanani lidzakhala lawo mpaka kalekale, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”+
8 Ine ndidzakulowetsani m’dziko limene ndinalumbirira+ Abulahamu, Isaki ndi Yakobo, nditakweza dzanja langa. Ndidzakupatsani dzikolo kukhala lanu.+ Ine ndine Yehova.’”+