Deuteronomo 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti ndinu anthu oyera+ kwa Yehova Mulungu wanu, ndipo Yehova wakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera,+ mwa anthu onse okhala padziko lapansi. Salimo 105:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamene anati: “Ndidzakupatsa dziko la Kanani+Kuti likhale gawo la cholowa chako.”+
2 Pakuti ndinu anthu oyera+ kwa Yehova Mulungu wanu, ndipo Yehova wakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera,+ mwa anthu onse okhala padziko lapansi.