Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu n’kumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako.”+ Pambuyo pake, iye anamanga pamalopo guwa lansembe la Yehova, yemwe anaonekera kwa iye.

  • Genesis 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pamenepo iye anakhulupirira mwa Yehova,+ ndipo Mulunguyo anamuona Abulamu ngati wolungama.+

  • Genesis 26:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ukhale ngati mlendo m’dzikoli,+ ndipo ndidzapitiriza kukhala nawe ndi kukudalitsa, chifukwa mayiko onsewa ndidzawapereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Ndidzakwaniritsa lumbiro limene ndinalumbirira Abulahamu bambo ako.+

  • Aheberi 11:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mwa chikhulupiriro, anakhala monga mlendo m’dziko la lonjezo ngati kuti akukhala m’dziko lachilendo.+ Ndipo anali kukhala m’mahema+ pamodzi ndi Isaki+ ndi Yakobo,+ anzake olandira nawo limodzi lonjezolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena