Aroma 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti Abulahamu kapena mbewu yake sanalonjezedwe kuti adzalandira dziko monga cholowa chawo chifukwa cha chilamulo ayi.+ Analandira lonjezolo chifukwa chakuti anali wolungama mwa chikhulupiriro.+ Aroma 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiye chifukwa chake “anaonedwa ngati wolungama.”+ Agalatiya 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zili monga mmene Abulahamu “anakhulupirira mwa Yehova, ndipo Mulunguyo anamuona Abulahamu ngati wolungama.”+
13 Pakuti Abulahamu kapena mbewu yake sanalonjezedwe kuti adzalandira dziko monga cholowa chawo chifukwa cha chilamulo ayi.+ Analandira lonjezolo chifukwa chakuti anali wolungama mwa chikhulupiriro.+
6 Zili monga mmene Abulahamu “anakhulupirira mwa Yehova, ndipo Mulunguyo anamuona Abulahamu ngati wolungama.”+