Genesis 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo iye anakhulupirira mwa Yehova,+ ndipo Mulunguyo anamuona Abulamu ngati wolungama.+ Aroma 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi lemba limati chiyani paja? Limati: “Abulahamu anakhulupirira mwa Yehova, ndipo anaonedwa ngati wolungama.”+ Yakobo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho linakwaniritsidwa lemba limene limati, “Abulahamu anakhulupirira mwa Yehova,* ndipo anaonedwa ngati wolungama,”+ choncho anatchedwa “bwenzi la Yehova.”+
3 Kodi lemba limati chiyani paja? Limati: “Abulahamu anakhulupirira mwa Yehova, ndipo anaonedwa ngati wolungama.”+
23 Choncho linakwaniritsidwa lemba limene limati, “Abulahamu anakhulupirira mwa Yehova,* ndipo anaonedwa ngati wolungama,”+ choncho anatchedwa “bwenzi la Yehova.”+