Ekisodo 16:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Aisiraeli anadya mana kwa zaka 40+ mpaka pamene analowa mʼdziko limene munkakhala anthu.+ Iwo ankadya mana mpaka pamene anafika mʼmalire a dziko la Kanani.+
35 Aisiraeli anadya mana kwa zaka 40+ mpaka pamene analowa mʼdziko limene munkakhala anthu.+ Iwo ankadya mana mpaka pamene anafika mʼmalire a dziko la Kanani.+