Ekisodo 16:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndipo ana a Isiraeli anadya mana kwa zaka 40+ mpaka pamene analowa m’dziko lokhalidwa ndi anthu.+ Mana ndiwo anali chakudya chawo mpaka pamene anafika m’malire a dziko la Kanani.+
35 Ndipo ana a Isiraeli anadya mana kwa zaka 40+ mpaka pamene analowa m’dziko lokhalidwa ndi anthu.+ Mana ndiwo anali chakudya chawo mpaka pamene anafika m’malire a dziko la Kanani.+