Deuteronomo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova Mulungu wanu wakudalitsani pa chilichonse chimene dzanja lanu likuchita.+ Iye akudziwa za kuyenda kwanu kudutsa m’chipululu chachikulu ichi. Yehova Mulungu wanu wakhala nanu zaka 40 zimenezi,+ ndipo simunasowe kanthu.”’+ Deuteronomo 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ‘Pamene ndinali kukutsogolerani kwa zaka 40 m’chipululu,+ zovala zanu sizinathe ndiponso nsapato zanu sizinathe kumapazi anu.+ Amosi 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ine ndinatulutsa anthu inu m’dziko la Iguputo+ ndi kukuyendetsani m’chipululu zaka 40+ kuti mukatenge dziko la Aamori.+
7 Yehova Mulungu wanu wakudalitsani pa chilichonse chimene dzanja lanu likuchita.+ Iye akudziwa za kuyenda kwanu kudutsa m’chipululu chachikulu ichi. Yehova Mulungu wanu wakhala nanu zaka 40 zimenezi,+ ndipo simunasowe kanthu.”’+
5 ‘Pamene ndinali kukutsogolerani kwa zaka 40 m’chipululu,+ zovala zanu sizinathe ndiponso nsapato zanu sizinathe kumapazi anu.+
10 Koma ine ndinatulutsa anthu inu m’dziko la Iguputo+ ndi kukuyendetsani m’chipululu zaka 40+ kuti mukatenge dziko la Aamori.+