Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno m’chaka cha 40,*+ m’mwezi wa 11, pa tsiku loyamba la mweziwo, Mose analankhula ndi ana a Isiraeli zonse zimene Yehova anamulamula kuti awauze.

  • Deuteronomo 8:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Muzikumbukira njira yonse imene Yehova Mulungu wanu anakuyendetsani m’chipululu zaka 40 zonsezi.+ Iye anakuyendetsani m’chipululu kuti akuphunzitseni kudzichepetsa,+ kukuyesani+ pofuna kudziwa zimene zinali mumtima mwanu,+ kuti aone ngati mukanasunga malamulo ake kapena ayi.

  • Amosi 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma ine ndinatulutsa anthu inu m’dziko la Iguputo+ ndi kukuyendetsani m’chipululu zaka 40+ kuti mukatenge dziko la Aamori.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena