Numeri 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anawakwiyira koopsa Aisiraeli ndipo anawachititsa kuzungulira m’chipululu zaka 40,+ mpaka m’badwo wonse wochita zoipa pamaso pa Yehova utatha.+ Numeri 33:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Wansembe Aroni anakwera m’phiri la Hora monga mmene Yehova anamulamulira, ndipo anamwalira ali m’phirimo. Anamwalira m’chaka cha 40 kuchokera pamene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo, m’mwezi wachisanu, pa tsiku loyamba la mweziwo.+
13 Yehova anawakwiyira koopsa Aisiraeli ndipo anawachititsa kuzungulira m’chipululu zaka 40,+ mpaka m’badwo wonse wochita zoipa pamaso pa Yehova utatha.+
38 Wansembe Aroni anakwera m’phiri la Hora monga mmene Yehova anamulamulira, ndipo anamwalira ali m’phirimo. Anamwalira m’chaka cha 40 kuchokera pamene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo, m’mwezi wachisanu, pa tsiku loyamba la mweziwo.+