Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 8:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Zovala zanu sizinathe ndipo mapazi anu sanatupe m’zaka 40 zimenezi.+

  • Nehemiya 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kwa zaka 40+ munawapatsa chakudya m’chipululu. Iwo sanasowe kanthu.+ Zovala zawo sizinathe+ ndipo mapazi awo sanatupe.+

  • Mateyu 6:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Choncho musamade nkhawa+ n’kumanena kuti, ‘Tidya chiyani?’ kapena, ‘Timwa chiyani?’ kapena, ‘Tivala chiyani?’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena