Luka 10:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Poyankha Ambuye anamuuza kuti: “Marita, Marita, ukuda nkhawa+ ndiponso kutanganidwa ndi zinthu zambiri.+ Luka 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho lekani kudera nkhawa za chimene mudzadya ndi chimene mudzamwa, ndipo siyani kuvutika mumtima.+
41 Poyankha Ambuye anamuuza kuti: “Marita, Marita, ukuda nkhawa+ ndiponso kutanganidwa ndi zinthu zambiri.+
29 Choncho lekani kudera nkhawa za chimene mudzadya ndi chimene mudzamwa, ndipo siyani kuvutika mumtima.+