Salimo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzawononga olankhula bodza.+Munthu wokhetsa magazi+ ndi wachinyengo,+ Yehova amaipidwa naye. Yesaya 59:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ife taphwanya malamulo ndipo tamukana Yehova.+ Tabwerera m’mbuyo n’kumusiya Mulungu wathu. Tanena zinthu zopondereza ena ndi zopanduka.+ Taganiza mawu achinyengo mumtima mwathu n’kumawalankhula chapansipansi.+ Hoseya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Efuraimu amalankhula mabodza okhaokha kwa ine.+ Kulikonse kumene ndingayang’ane ndikuona chinyengo cha Isiraeli, koma Yuda akuyendabe ndi Mulungu+ ndipo iye ndi wokhulupirika kwa Woyera Koposa.”
13 Ife taphwanya malamulo ndipo tamukana Yehova.+ Tabwerera m’mbuyo n’kumusiya Mulungu wathu. Tanena zinthu zopondereza ena ndi zopanduka.+ Taganiza mawu achinyengo mumtima mwathu n’kumawalankhula chapansipansi.+
12 “Efuraimu amalankhula mabodza okhaokha kwa ine.+ Kulikonse kumene ndingayang’ane ndikuona chinyengo cha Isiraeli, koma Yuda akuyendabe ndi Mulungu+ ndipo iye ndi wokhulupirika kwa Woyera Koposa.”