2 Mafumu 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anadalira Yehova Mulungu wa Isiraeli.+ Panalibenso mfumu ina yofanana naye pamafumu onse a Yuda+ amene anakhalapo iye asanakhale mfumu, ngakhalenso amene anakhalapo iye atafa.+ 2 Mbiri 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonse zimene Davide kholo lake anachita.+ Salimo 89:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti chishango chathu ndi chochokera kwa Yehova,+Ndipo mfumu yathu ndi yochokera kwa Woyera wa Isiraeli.+ Hoseya 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita dama,+ Yuda asakhale wolakwa+ ndipo anthu inu musabwere ku Giligala.+ Musapitenso ku Beti-aveni+ kapena kulumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’+
5 Iye anadalira Yehova Mulungu wa Isiraeli.+ Panalibenso mfumu ina yofanana naye pamafumu onse a Yuda+ amene anakhalapo iye asanakhale mfumu, ngakhalenso amene anakhalapo iye atafa.+
2 Iye anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonse zimene Davide kholo lake anachita.+
18 Pakuti chishango chathu ndi chochokera kwa Yehova,+Ndipo mfumu yathu ndi yochokera kwa Woyera wa Isiraeli.+
15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita dama,+ Yuda asakhale wolakwa+ ndipo anthu inu musabwere ku Giligala.+ Musapitenso ku Beti-aveni+ kapena kulumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’+