Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 78:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Koma iwo anali kufuna kum’pusitsa ndi pakamwa pawo.+

      Ndi lilime lawo anali kufuna kunena bodza kwa iye.+

  • Yesaya 29:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova wanena kuti: “Popeza anthu awa ayandikira kwa ine ndi pakamwa pawo pokha, ndipo andilemekeza ndi milomo yawo yokha+ koma mtima wawo auika kutali ndi ine,+ ndiponso amangophunzira malamulo a anthu n’kumaganiza kuti kuchita zimenezo ndiye kundiopa,+

  • Mika 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anthu olemera a mumzindawo amakonda kuchita zachiwawa. Anthu okhalamo akulankhula zonama+ ndipo lilime la m’kamwa mwawo ndi lachinyengo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena