Salimo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’kamwa mwake mwadzaza matemberero, chinyengo ndi kupondereza ena.+Pansi pa lilime lake pamatuluka mavuto ndi zopweteka ena.+ Salimo 59:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa cha tchimo la pakamwa pawo, ndi mawu a pamilomo yawo.+Agwidwe chifukwa cha kunyada kwawo,+Chifukwa cha kutukwana ndi chinyengo zimene amachita mobwerezabwereza.
7 M’kamwa mwake mwadzaza matemberero, chinyengo ndi kupondereza ena.+Pansi pa lilime lake pamatuluka mavuto ndi zopweteka ena.+
12 Chifukwa cha tchimo la pakamwa pawo, ndi mawu a pamilomo yawo.+Agwidwe chifukwa cha kunyada kwawo,+Chifukwa cha kutukwana ndi chinyengo zimene amachita mobwerezabwereza.