Ekisodo 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno anatenga buku la pangano+ ndi kuwerengera anthuwo kuti amve.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+ 1 Samueli 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthu akachimwira mnzake,+ Mulungu adzam’pepesera,+ koma kodi akachimwira Yehova,+ angamupempherere ndani?”+ Koma anawo sanali kumvera bambo awo+ chifukwa tsopano Yehova anali atatsimikiza mtima kuti awaphe.+
7 Ndiyeno anatenga buku la pangano+ ndi kuwerengera anthuwo kuti amve.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+
25 Munthu akachimwira mnzake,+ Mulungu adzam’pepesera,+ koma kodi akachimwira Yehova,+ angamupempherere ndani?”+ Koma anawo sanali kumvera bambo awo+ chifukwa tsopano Yehova anali atatsimikiza mtima kuti awaphe.+