Deuteronomo 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu amene adzadzikuza mwa kusamvera wansembe amene akutumikira Yehova Mulungu wako kapena mwa kusamvera woweruza,+ munthu ameneyo afe ndithu.+ Muzichotsa woipayo mu Isiraeli.+ 1 Mafumu 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Munthu akachimwira mnzake,+ wochimwiridwayo n’kulumbiritsa*+ wochimwayo pofuna kutsimikiza kuti sanachimwedi, ndiyeno wochimwayo akabwera patsogolo pa guwa lansembe m’nyumba ino chifukwa cha zimene analumbira,
12 Munthu amene adzadzikuza mwa kusamvera wansembe amene akutumikira Yehova Mulungu wako kapena mwa kusamvera woweruza,+ munthu ameneyo afe ndithu.+ Muzichotsa woipayo mu Isiraeli.+
31 “Munthu akachimwira mnzake,+ wochimwiridwayo n’kulumbiritsa*+ wochimwayo pofuna kutsimikiza kuti sanachimwedi, ndiyeno wochimwayo akabwera patsogolo pa guwa lansembe m’nyumba ino chifukwa cha zimene analumbira,