Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 7:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Usabweretse m’nyumba mwako zinthu zonyansa kuti iwenso ungawonongedwe mofanana ndi zinthuzo. Uzinyansidwa nazo kwambiri ndi kuipidwa nazo+ chifukwa zinthu zimenezi ndi zoyenera kuwonongedwa.+

  • Yoswa 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma zinthu zoyenera kuwonongedwa musamale nazo,+ kuopera kuti mungazikhumbire+ n’kutengako zinthuzo,+ n’kuchititsa msasa wa Isiraeli nawonso kukhala chinthu choyenera kuwonongedwa ndi kunyanyalidwa.+

  • Yoswa 7:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Aisiraeli achimwa, ndiponso aphwanya pangano+ limene ndinawalamula kuti alisunge. Iwo atenga zina mwa zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Aba+ zinthuzo ndi kuzibisa+ pakati pa katundu wawo.+

  • Yoswa 22:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kodi Akani+ mwana wa Zera sanachite zosakhulupirika pa chinthu choyenera kuwonongedwa? Kodi mkwiyo sunagwere khamu lonse la Isiraeli?+ Komatu iye sanafe yekha chifukwa cha cholakwa chakecho.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena