Yoswa 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aisiraeli achimwa, ndiponso aphwanya pangano+ limene ndinawalamula kuti alisunge. Iwo atenga zina mwa zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Aba+ zinthuzo ndi kuzibisa+ pakati pa katundu wawo.+ Yoswa 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amene apezeke ndi zinthu zoyenera kuwonongedwazo, adzatenthedwa ndi moto,+ iye limodzi ndi banja lake ndi zonse ali nazo. Adzatenthedwa chifukwa waphwanya pangano la Yehova,+ ndiponso wachita cholakwa chochititsa manyazi mu Isiraeli.”’”+
11 Aisiraeli achimwa, ndiponso aphwanya pangano+ limene ndinawalamula kuti alisunge. Iwo atenga zina mwa zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Aba+ zinthuzo ndi kuzibisa+ pakati pa katundu wawo.+
15 Amene apezeke ndi zinthu zoyenera kuwonongedwazo, adzatenthedwa ndi moto,+ iye limodzi ndi banja lake ndi zonse ali nazo. Adzatenthedwa chifukwa waphwanya pangano la Yehova,+ ndiponso wachita cholakwa chochititsa manyazi mu Isiraeli.”’”+