Oweruza 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho ndinatenga mdzakazi wanga ndi kum’duladula, n’kutumiza ziwalozo m’dera lililonse la cholowa cha Isiraeli.+ Ndinatero chifukwa iwo anachita khalidwe lotayirira+ komanso chinthu chopusa ndi chochititsa manyazi mu Isiraeli.+ 2 Samueli 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Tamara anamuuza kuti: “Ayi, m’bale wanga! Usandichititse manyazi,+ chifukwa zimenezi n’zachilendo mu Isiraeli.+ Usachite chinthu chopusa, chochititsa manyazi ngati chimenechi.+
6 Choncho ndinatenga mdzakazi wanga ndi kum’duladula, n’kutumiza ziwalozo m’dera lililonse la cholowa cha Isiraeli.+ Ndinatero chifukwa iwo anachita khalidwe lotayirira+ komanso chinthu chopusa ndi chochititsa manyazi mu Isiraeli.+
12 Koma Tamara anamuuza kuti: “Ayi, m’bale wanga! Usandichititse manyazi,+ chifukwa zimenezi n’zachilendo mu Isiraeli.+ Usachite chinthu chopusa, chochititsa manyazi ngati chimenechi.+