Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “‘Musaipitse mwana wanu wamkazi mwa kum’sandutsa hule,+ kuti dziko lingachite uhule ndi kudzaza makhalidwe otayirira.+

  • Levitiko 20:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Mwamuna akakwatira mkazi n’kugonanso ndi mayi a mkaziyo, limenelo ndi khalidwe lotayirira.+ Aziphedwa ndi kutenthedwa,+ onse mwamunayo ndi akaziwo, kuti khalidwe lotayirira+ lisapitirire pakati panu.

  • Salimo 119:150
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 150 Okonda kuchita khalidwe lotayirira+ abwera pafupi ndi ine.

      Iwo atalikirana kwambiri ndi chilamulo chanu.+

  • Miyambo 10:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kwa wopusa, kusonyeza khalidwe lotayirira kuli ngati masewera,+ koma nzeru zimakhala ndi munthu wozindikira.+

  • 1 Petulo 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti nthawi+ imene yapitayi inali yokwanira kwa inu kuchita chifuniro cha anthu a m’dzikoli+ pamene munali kuchita zinthu zosonyeza khalidwe lotayirira,+ zilakolako zoipa, kumwa vinyo mopitirira muyezo,+ maphwando aphokoso, kumwa kwa mpikisano, ndi kupembedza mafano kosaloleka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena