Aroma 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+ Aroma 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi pa nthawiyo munali kukhala ndi zipatso zotani?+ Zinali zinthu+ zimene tsopano mumachita nazo manyazi. Ndipo pothera pake pa zinthu zimenezo ndi imfa.+ Aefeso 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho, ndikunena izi ndi kuzichitira umboni mwa Ambuye, kuti musamayendenso monga mmene anthu a mitundu ina+ amayendera, potsatira maganizo awo opanda pake.+ Tito 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ngakhale ife nthawi inayake tinali opanda nzeru, osamvera, osocheretsedwa, akapolo a zilakolako ndi zosangalatsa zosiyanasiyana, ochita zoipa, akaduka, onyansa ndiponso achidani.+
28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+
21 Kodi pa nthawiyo munali kukhala ndi zipatso zotani?+ Zinali zinthu+ zimene tsopano mumachita nazo manyazi. Ndipo pothera pake pa zinthu zimenezo ndi imfa.+
17 Choncho, ndikunena izi ndi kuzichitira umboni mwa Ambuye, kuti musamayendenso monga mmene anthu a mitundu ina+ amayendera, potsatira maganizo awo opanda pake.+
3 Pakuti ngakhale ife nthawi inayake tinali opanda nzeru, osamvera, osocheretsedwa, akapolo a zilakolako ndi zosangalatsa zosiyanasiyana, ochita zoipa, akaduka, onyansa ndiponso achidani.+