Aroma 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiye zili bwanji pamenepa? Chimene Aisiraeli akuchifunitsitsa sanachipeze,+ koma anthu osankhidwa+ ndi amene anachipeza. Enawo anaumitsa mitima yawo+ 2 Akorinto 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo maganizo awo anachita khungu.+ Pakuti mpaka lero, nsaluyo imakhalabe yophimba powerenga pangano lakale,+ chifukwa imachotsedwa kudzera mwa Khristu basi.+
7 Ndiye zili bwanji pamenepa? Chimene Aisiraeli akuchifunitsitsa sanachipeze,+ koma anthu osankhidwa+ ndi amene anachipeza. Enawo anaumitsa mitima yawo+
14 Ndipo maganizo awo anachita khungu.+ Pakuti mpaka lero, nsaluyo imakhalabe yophimba powerenga pangano lakale,+ chifukwa imachotsedwa kudzera mwa Khristu basi.+