Yohane 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anabwera kudziko lakwawo, koma anthu akwawo enieniwo sanamulandire.+ Aroma 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma ngakhale kuti Aisiraeli anali kutsatira lamulo la chilungamo, sanalipeze lamulolo.+