Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 20:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Mwamuna akakwatira mkazi n’kugonanso ndi mayi a mkaziyo, limenelo ndi khalidwe lotayirira.+ Aziphedwa ndi kutenthedwa,+ onse mwamunayo ndi akaziwo, kuti khalidwe lotayirira+ lisapitirire pakati panu.

  • Miyambo 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Khalidwe lotayirira lobwera chifukwa cha kupusa limakhala tchimo,+ ndipo munthu wonyoza, anthu amanyansidwa naye.+

  • Yeremiya 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno Yehova anayankha kuti: “Chifukwa chakuti iwo asiya chilamulo changa chimene ndinawapatsa kuti chizikhala pamaso pawo, komanso chifukwa chakuti iwo sanamvere mawu anga ndi kuwatsatira,+

  • Aroma 1:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Amenewa ngakhale kuti amalidziwa bwino lamulo lolungama la Mulungu,+ lakuti amene amachita zinthu zimenezi n’ngoyenera imfa,+ iwo amapitiriza kuzichita. Kuwonjezera apo, amagwirizananso+ ndi anthu amene amachita zimenezo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena