Levitiko 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wotemberera dzina la Mulungu uja, mum’tulutsire kunja kwa msasa.+ Onse amene anamumva aike manja awo+ pamutu pake ndipo khamu lonse lim’ponye miyala.+ Yoswa 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu aliyense wopandukira malamulo anu,+ ndi wosamvera mawu anu pa chilichonse chimene mungamulamule, ameneyo aphedwe.+ Inuyo mukhale wolimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.”+
14 “Munthu wotemberera dzina la Mulungu uja, mum’tulutsire kunja kwa msasa.+ Onse amene anamumva aike manja awo+ pamutu pake ndipo khamu lonse lim’ponye miyala.+
18 Munthu aliyense wopandukira malamulo anu,+ ndi wosamvera mawu anu pa chilichonse chimene mungamulamule, ameneyo aphedwe.+ Inuyo mukhale wolimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.”+