Deuteronomo 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma umuphe ndithu.+ Dzanja lako lizikhala loyamba kum’ponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+ Deuteronomo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dzanja la mbonizo lizikhala loyamba kum’ponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+ Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+
9 Koma umuphe ndithu.+ Dzanja lako lizikhala loyamba kum’ponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+
7 Dzanja la mbonizo lizikhala loyamba kum’ponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+ Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+