Yoswa 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi Akani+ mwana wa Zera sanachite zosakhulupirika pa chinthu choyenera kuwonongedwa? Kodi mkwiyo sunagwere khamu lonse la Isiraeli?+ Komatu iye sanafe yekha chifukwa cha cholakwa chakecho.’”+ 1 Mbiri 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwana wa Karami+ anali Akari,* amene anachititsa Isiraeli kunyanyalidwa.+ Iye anachita zinthu zosakhulupirika zokhudzana ndi chinthu choyenera kuwonongedwa.+
20 Kodi Akani+ mwana wa Zera sanachite zosakhulupirika pa chinthu choyenera kuwonongedwa? Kodi mkwiyo sunagwere khamu lonse la Isiraeli?+ Komatu iye sanafe yekha chifukwa cha cholakwa chakecho.’”+
7 Mwana wa Karami+ anali Akari,* amene anachititsa Isiraeli kunyanyalidwa.+ Iye anachita zinthu zosakhulupirika zokhudzana ndi chinthu choyenera kuwonongedwa.+