Miyambo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umu ndi mmene zimakhalira njira za aliyense wopeza phindu mwachinyengo.+ Phindulo limachotsa moyo wa eni akewo.+ Aroma 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso+ imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+
19 Umu ndi mmene zimakhalira njira za aliyense wopeza phindu mwachinyengo.+ Phindulo limachotsa moyo wa eni akewo.+
23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso+ imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+