Deuteronomo 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Munthu asalande mnzake mphero kapena mwala woperera monga chikole.+ Kumulanda zimenezi monga chikole ndiko kumulanda moyo. Yobu 31:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ngati ndadya zipatso zake osapereka ndalama,+Ndipo ndachititsa moyo wa olima ake kupumira m’mwamba,+
6 “Munthu asalande mnzake mphero kapena mwala woperera monga chikole.+ Kumulanda zimenezi monga chikole ndiko kumulanda moyo.
39 Ngati ndadya zipatso zake osapereka ndalama,+Ndipo ndachititsa moyo wa olima ake kupumira m’mwamba,+