Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kenako Gehazi,+ amene anali kutumikira Elisa, munthu wa Mulungu woona+ uja, ananena mumtima mwake kuti: “Mbuyanga wangomusiya Namani+ Msiriya uja osalandira zimene anabweretsa. Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ ndim’thamangira kuti ndikatengeko zinthu zina kwa iye.”+

  • Miyambo 15:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Munthu wopeza phindu mwachinyengo amabweretsa tsoka panyumba pake,+ koma wodana ndi ziphuphu ndi amene adzakhalebe ndi moyo.+

  • Mika 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Atsogoleri a mumzindawo saweruza asanalandire chiphuphu+ ndipo ansembe ake amaphunzitsa kuti apeze malipiro.+ Aneneri ake amalosera kuti apeze ndalama.+ Komatu iwo amadalira Yehova ndipo amanena kuti: “Kodi Yehova sali pakati pathu?+ Choncho tsoka silidzatigwera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena