-
2 Mafumu 5:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Tsopano munthu winawake dzina lake Namani,+ mkulu wa gulu la asilikali a mfumu ya Siriya, anakhala munthu wofunika pamaso pa mbuye wake. Iye anali wolemekezeka, chifukwa Yehova anapulumutsa Siriya+ kudzera mwa iyeyo. Munthuyo anasonyeza kuti anali wamphamvu ndi wolimba mtima, ngakhale kuti anali wakhate.
-