2 Mafumu 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Namani atamva zimenezi, anatsetserekera ku Yorodano n’kukamira maulendo 7, mogwirizana ndi mawu a munthu wa Mulungu woona+ uja. Pambuyo pake, mnofu wake unabwerera mwakale moti unakhala ngati mnofu wa kamnyamata,+ ndipo anakhala woyera.+ Luka 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiponso, munali akhate ambiri mu Isiraeli m’nthawi ya mneneri Elisa. Komabe palibe aliyense wa iwo amene anayeretsedwa, koma Namani, mwamuna wa ku Siriya.”+
14 Namani atamva zimenezi, anatsetserekera ku Yorodano n’kukamira maulendo 7, mogwirizana ndi mawu a munthu wa Mulungu woona+ uja. Pambuyo pake, mnofu wake unabwerera mwakale moti unakhala ngati mnofu wa kamnyamata,+ ndipo anakhala woyera.+
27 Ndiponso, munali akhate ambiri mu Isiraeli m’nthawi ya mneneri Elisa. Komabe palibe aliyense wa iwo amene anayeretsedwa, koma Namani, mwamuna wa ku Siriya.”+